Afilipi 1:3 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Ndimayamika Mulungu wanga nthawi zonse ndikakumbukira inu. Onani mutuwoBuku Lopatulika3 Ndiyamika Mulungu wanga pokumbukira inu ponse; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndiyamika Mulungu wanga pokumbukira inu ponse; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Ndimayamika Mulungu wanga nthaŵi zonse ndikamakukumbukirani. Onani mutuwo |