2 Samueli 1:3 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Davide anamufunsa iye kuti, “Kodi iwe wachokera kuti?” Iye anayankha kuti, “Ine ndathawa ku misasa ya Aisraeli.” Onani mutuwoBuku Lopatulika3 Ndipo Davide ananena naye, Ufumira kuti iwe? Iye nanena naye, Ndapulumuka ku zithando za Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo Davide ananena naye, Ufumira kuti iwe? Iye nanena naye, Ndapulumuka ku zithando za Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Davide adamufunsa kuti, “Ukuchokera kuti?” Iye adayankha kuti, “Ndathaŵa ku zithando zankhondo za Aisraele.” Onani mutuwo |