Zekariya 7:9 - Buku Lopatulika9 Watero Yehova wa makamu, kuti, Weruzani chiweruzo choona, nimuchitire yense mnzake chifundo ndi ukoma mtima; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Watero Yehova wa makamu, kuti, Weruzani chiweruzo choona, nimuchitire yense mnzake chifundo ndi ukoma mtima; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 “Zimene ndikunena Ine Chauta Wamphamvuzonse ndi izi: Muziweruzana molungama. Muzimverana chisoni ndi kuchitirana chifundo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 “Yehova Wamphamvuzonse akuti, ‘Muziweruza molungama; muzichitirana chifundo ndi kumverana chisoni. Onani mutuwo |