Zekariya 4:11 - Buku Lopatulika11 Pamenepo ndinayankha, ndinati kwa iye, Mitengo iyi iwiri ya azitona kulamanja ndi kulamanzere kwa choikaponyali nchiyani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Pamenepo ndinayankha, ndinati kwa iye, Mitengo iyi iwiri ya azitona kulamanja ndi kulamanzere kwa choikapo nyali nchiyani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Tsono ndidamufunsa munthuyo kuti, “Nanga mitengo iŵiri ya olivi ili kumanja ndi kumanzere kwa choikaponyalecho ikutanthauza chiyani?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Kenaka ndinafunsa mngelo uja kuti, “Kodi mitengo ya olivi iwiri ili kumanja ndi kumanzere kwa choyikapo nyalechi ikutanthauza chiyani?” Onani mutuwo |