Zekariya 2:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo Yehova adzalandira cholowa chake Yuda, ngati gawo lake m'dziko lopatulikalo, nadzasankhanso Yerusalemu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo Yehova adzalandira cholowa chake Yuda, ngati gawo lake m'dziko lopatulikalo, nadzasankhanso Yerusalemu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Iyeyo adzamtenganso Yuda kuti akhale chuma chake m'dziko lopatulika, ndipo Yerusalemu adzakhala mzinda wake wapamtima. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Yehova adzachititsa kuti Yuda akhale chuma chake mʼdziko lopatulika ndipo adzasankhanso Yerusalemu. Onani mutuwo |