Zekariya 13:5 - Buku Lopatulika5 koma adzati, Sindili mneneri, ndili wolima munda; pakuti munthu anandiyesa kapolo kuyambira ubwana wanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 koma adzati, Sindili mneneri, ndili wolima munda; pakuti munthu anandiyesa kapolo kuyambira ubwana wanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Koma adzati, ‘Sindine mneneri ai. Ndine mlimi, poti ndakhala ndikulima munda kuyambira ubwana wanga.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Iye adzati, ‘Sindine mneneri. Ndine mlimi; ndakhala ndi kulima munda kuyambira ubwana wanga.’ Onani mutuwo |