Yuda 1:13 - Buku Lopatulika13 mafunde oopsa a nyanja, akuwinduka thovu la manyazi a iwo okha; nyenyezi zosokera, zimene mdima wakuda bii udazisungikira kosatha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 mafunde oopsa a nyanja, akuwinduka thovu la manyazi a iwo okha; nyenyezi zosokera, zimene mdima wakuda bii udazisungikira kosatha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Ali ngati mafunde aukali apanyanja, amene amatulutsa thovu la zonyansa zao. Ali ngati nyenyezi zosokera, ndipo Mulungu akuŵasungira mdima wandiweyani mpaka muyaya. Mbiri iyi idadziŵika pakati pa Aisraele, koma siinalembedwe m'Chipangano Chakale. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Iwowa ali ngati mafunde awukali apanyanja, amene amatulutsa thovu la zonyansa zawo. Amenewa ali ngati nyenyezi zosochera, ndipo Mulungu akuwasungira mdima wandiweyani mpaka muyaya. Onani mutuwo |