Yohane 8:5 - Buku Lopatulika5 Koma m'chilamulo Mose anatilamula, tiwaponye miyala otere. Chifukwa chake Inu munena chiyani za iye? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Koma m'chilamulo Mose anatilamula, tiwaponye miyala otere. Chifukwa chake Inu munena chiyani za iye? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Paja m'buku la Malamulo Mose adatilamula kuti munthu wotere tizipha pakumponya miyala. Nanga Inuyo mukuti chiyani pamenepa?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Mʼmalamulo a Mose anatilamulira kuti akazi otere tiwagende ndi miyala. Tsopano Inu mukuti chiyani?” Onani mutuwo |