Yohane 8:13 - Buku Lopatulika13 Chifukwa chake Afarisi anati kwa Iye, Muchita umboni wa Inu nokha; umboni wanu suli woona. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Chifukwa chake Afarisi anati kwa Iye, Muchita umboni wa Inu nokha; umboni wanu suli woona. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Apo Afarisi adamuuza kuti, “Ukudzichitira wekha umboni. Umboni wakowo ngwosakwanira.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Afarisi anamutsutsa Iye nati, “Iwe ukudzichitira umboni wa Iwe mwini, umboni wako siwoona.” Onani mutuwo |