Yohane 6:52 - Buku Lopatulika52 Pamenepo Ayuda anatetana wina ndi mnzake ndi kunena, Akhoza bwanji ameneyu kutipatsa ife kudya thupi lake? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201452 Pamenepo Ayuda anatetana wina ndi mnzake ndi kunena, Akhoza bwanji ameneyu kutipatsa ife kudya thupi lake? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa52 Pamenepo Ayuda aja adayamba kukangana okhaokha, ankati, “Munthu ameneyu angathe bwanji kutipatsa thupi lake kuti tidye?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero52 Kenaka Ayuda anayamba kutsutsana kwambiri pakati pawo kuti, “Kodi munthu uyu angathe kutipatsa bwanji thupi lake kuti tidye?” Onani mutuwo |