Yohane 4:1 - Buku Lopatulika1 Chifukwa chake pamene Ambuye anadziwa kuti Afarisi adamva kuti Yesu anayesa anthu ophunzira, nawabatiza koposa Yohane Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Chifukwa chake pamene Ambuye anadziwa kuti Afarisi adamva kuti Yesu anayesa anthu ophunzira, nawabatiza koposa Yohane Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Afarisi adamva kuti Yesu akukopa ndi kubatiza ophunzira ambiri koposa Yohane. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Yesu atazindikira kuti Afarisi amva zoti Iye ankapeza ndi kubatiza ophunzira ambiri kupambana Yohane, Onani mutuwo |