Yohane 3:30 - Buku Lopatulika30 Iyeyo ayenera kukula koma ine ndichepe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Iyeyo ayenera kukula koma ine ndichepe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Iye uja ayenera kumakula, ine nkumachepa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Nʼkoyenera kuti Iyeyo akule, ine ndichepe. Onani mutuwo |