Yohane 3:17 - Buku Lopatulika17 Pakuti Mulungu sanatume Mwana wake kudziko lapansi, kuti akaweruze dziko lapansi, koma kuti dziko lapansi likapulumutsidwe ndi Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Pakuti Mulungu sanatume Mwana wake kudziko lapansi, kuti akaweruze dziko lapansi, koma kuti dziko lapansi likapulumutsidwe ndi Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Mulungu adatuma Mwana wakeyo pansi pano, osati kuti adzazenge anthu mlandu, koma kuti adzaŵapulumutse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Pakuti Mulungu sanatume Mwana wake ku dziko lapansi, kuti akaweruze, koma kuti akapulumutse dziko lapansi. Onani mutuwo |