Yohane 2:7 - Buku Lopatulika7 Yesu ananena nao, Dzazani mitsukoyo ndi madzi. Naidzaza, ndendende. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Yesu ananena nao, Dzazani mitsukoyo ndi madzi. Naidzaza, ndendende. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Tsono Yesu adauza anyamata aja kuti, “Dzazani mbiyazi ndi madzi.” Ndipo adazidzaza mpaka m'milomo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Yesu anati kwa antchitowo, “Dzazani madzi mʼmitsukoyi,” ndipo iwo anadzaza ndendende. Onani mutuwo |