Yohane 18:21 - Buku Lopatulika21 Undifunsiranji Ine? Funsa iwo amene adamva chimene ndinalankhula nao; taona, amenewo adziwa chimene ndinanena Ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Undifunsiranji Ine? Funsa iwo amene adamva chimene ndinalankhula nao; taona, amenewo adziwa chimene ndinanena Ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Nanga tsono mukundifunsiranji Ineyo? Funsani amene adamva zomwe ndinkaŵauza. Iwowo akudziŵa zimene ndinkanena.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Nʼchifukwa chiyani mukundifunsa Ine? Afunseni amene amamva. Zoonadi akudziwa zimene Ine ndinanena.” Onani mutuwo |