Yohane 16:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo izi adzachita, chifukwa sanadziwe Atate, kapena Ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo izi adzachita, chifukwa sanadziwa Atate, kapena Ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Adzachita zimenezi chifukwa sadadziŵe Atate kapenanso Ine. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Iwo adzachita zoterozo chifukwa sanadziwe Atate kapena Inenso. Onani mutuwo |