Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 15:3 - Buku Lopatulika

3 Mwakhala okonzeka tsopano inu chifukwa cha mau amene ndalankhula ndi inu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Mwakhala okonzeka tsopano inu chifukwa cha mau amene ndalankhula ndi inu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Inu mwayera kale chifukwa cha mau amene ndakuuzani.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Inu ndinu oyera kale chifukwa cha mawu amene ndayankhula inu.

Onani mutuwo Koperani




Yohane 15:3
6 Mawu Ofanana  

Yesu ananena naye, Amene anatha kusamba alibe kusowa koma kusamba mapazi, koma ayera monse: ndipo inu ndinu oyera, koma si nonse ai.


Nthambi iliyonse ya mwa Ine yosabala chipatso, aichotsa; ndi iliyonse yakubala chipatso, aisadza, kuti ikabale chipatso chochuluka.


Patulani iwo m'choonadi; mau anu ndi choonadi.


Ndipo chifukwa cha iwo Ine ndidzipatula ndekha kuti iwonso akhale opatulidwa m'choonadi.


kuti akampatule, atamyeretsa ndi kumsambitsa madzi ndi mau;


Popeza mwayeretsa moyo wanu pakumvera choonadi kuti mukakonde abale ndi chikondi chosanyenga, mukondane kwenikweni kuchokera kumtima;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa