Yohane 10:2 - Buku Lopatulika2 Koma iye wakulowera pakhomo, ndiye mbusa wa nkhosa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Koma iye wakulowera pakhomo, ndiye mbusa wa nkhosa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Koma munthu woloŵera pa khomo ndiye mbusa wa nkhosazo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Munthu amene amalowera pa khomo ndi mʼbusa wankhosazo. Onani mutuwo |