Yohane 1:26 - Buku Lopatulika26 Yohane anawayankha, nati, Ine ndibatiza ndi madzi; pakati pa inu paimirira amene simumdziwa, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Yohane anawayankha, nati, Ine ndibatiza ndi madzi; pakati pa inu paimirira amene simumdziwa, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Yohane adaŵayankha kuti, “Ine ndimabatiza ndi madzi, koma pakati panupa pali wina amene inu simukumdziŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Yohane anayankha kuti, “Ine ndimabatiza ndi madzi, koma pakati panu payima amene simukumudziwa. Onani mutuwo |