Yohane 1:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo anavomera, wosakana; nalola kuti, Sindine Khristu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo anavomera, wosakana; nalola kuti, Sindine Khristu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Iye adayankha mosabisa konse, adanenetsa ndithu kuti, “Inetu sindine Mpulumutsi wolonjezedwa uja ai.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Iye sanalephere kuvomereza, koma iye anavomereza momasuka kuti, “Ine sindine Khristu.” Onani mutuwo |