Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yeremiya 6:3 - Buku Lopatulika

3 Abusa ndi nkhosa zao adzadza kwa iye; adzamanga mahema ao pomzinga iye; adzadya yense pokhala pake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Abusa ndi nkhosa zao adzadza kwa iye; adzamanga mahema ao pomzinga iye; adzadya yense pokhala pake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Mafumu adzabwera ndi asilikali ao. Adzamanga zithando momzinga Yerusalemu, ndipo aliyense adzakhazika anthu ake pamalo pake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Abusa ndi nkhosa zawo adzabwera kudzalimbana nawo; adzamanga matenti awo mowuzinga, ndipo aliyense adzakhazika anthu ake pamalo pake.”

Onani mutuwo Koperani




Yeremiya 6:3
8 Mawu Ofanana  

Ndipo Yehova anamtumizira magulu a Ababiloni, ndi magulu a Aaramu, ndi magulu a Amowabu, ndi magulu a ana a Amoni, nawatumiza pa Yuda kuliononga, monga mwa mau a Yehova adawanena ndi dzanja la atumiki ake aneneriwo.


Abusa ambiri aononga munda wanga wampesa, apondereza gawo langa, pondikondweretsa apayesa chipululu chopanda kanthu.


Abusa ako aodzera, mfumu ya ku Asiriya; omveka ako apumula; anthu ako amwazika pamapiri, ndipo palibe wakuwasonkhanitsa.


Pakuti masiku adzakudzera, ndipo adani ako adzakuzingira linga, nadzakuzungulira iwe kwete, nadzakutsekereza ponsepo;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa