Yeremiya 41:3 - Buku Lopatulika3 Ismaele naphanso Ayuda onse okhala naye Gedaliya pa Mizipa, ndi Ababiloni amene anakomana nao komweko, amuna a nkhondo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ismaele naphanso Ayuda onse okhala naye Gedaliya pa Mizipa, ndi Ababiloni amene anakomana nao komweko, amuna a nkhondo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Ismaele adaphanso Ayuda onse amene anali ku Mizipa ndiponso ankhondo a Ababiloni amene anali kumeneko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Ismaeli anaphanso Ayuda onse amene anali pamodzi ndi Gedaliya ku Mizipa, kuphatikizanso asilikali a Ababuloni amene anali ku Mizipako. Onani mutuwo |