Yeremiya 10:2 - Buku Lopatulika2 Atero Yehova, Musaphunzire njira ya amitundu, musaope zizindikiro za m'thambo; pakuti amitundu aziopa izo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Atero Yehova, Musaphunzire njira ya amitundu, musaope zizindikiro za m'thambo; pakuti amitundu aziopa izo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Chauta akuti, “Musatsate makhalidwe a anthu a mitundu ina. Musachite mantha ndi zizindikiro zozizwitsa zamumlengalenga, ngakhale anthu a mitundu ina amachita nazo mantha zimenezi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Yehova akuti, “Musatsatire makhalidwe a anthu a mitundu ina kapena kuchita mantha ndi zizindikiro zamlengalenga, ngakhale anthu a mitundu ina amachita nazo mantha. Onani mutuwo |