Yeremiya 1:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo ndinati, Ha, Ambuye Mulungu! Taonani, sindithai kunena pakuti ndili mwana. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo ndinati, Ha, Ambuye Mulungu! Taonani, sindithai kunena pakuti ndili mwana. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Ine ndidati, “Ha, Ambuye Chauta! Ine ndine mwana, kulankhula sindidziŵa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Ine ndinati, “Haa! Ambuye Yehova, ine sinditha kuyankhula; popeza ndikanali wamngʼono.” Onani mutuwo |