Yakobo 2:4 - Buku Lopatulika4 kodi simunasiyanitse mwa inu nokha, ndi kukhala oweruza oganizira zoipa? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 kodi simunasiyanitsa mwa inu nokha, ndi kukhala oweruza oganizira zoipa? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Limenelotu ndi tsankho pakati pa inu nokhanokha, ndipo inuyo mwasanduka oweruza a maganizo oipa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 kodi simunachite tsankho pakati panu ndi kukhala oweruza a maganizo oyipa? Onani mutuwo |