Tito 3:6 - Buku Lopatulika6 amene anatsanulira pa ife mochulukira, mwa Yesu Khristu Mpulumutsi wathu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 amene anatsanulira pa ife mochulukira, mwa Yesu Khristu Mpulumutsi wathu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Mwa Yesu Khristu, Mpulumutsi wathu, Mulungu adatipatsa Mzimu Woyerayo moolowa manja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 amene anatipatsa mowolowamanja kudzera mwa Yesu Khristu Mpulumutsi wathu, Onani mutuwo |