Tito 3:4 - Buku Lopatulika4 Koma pamene kukoma mtima, ndi chikondi cha pa anthu, cha Mpulumutsi wathu Mulungu zidanoneka, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Koma pamene kukoma mtima, ndi chikondi cha pa anthu, cha Mpulumutsi wathu Mulungu zidanoneka, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Koma pamenepo Mulungu Mpulumutsi wathu adaonetsa kukoma kwake ndiponso chifundo chokonda anthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Koma kukoma mtima ndi chikondi cha Mulungu Mpulumutsi wathu chitaonekera, Onani mutuwo |