Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Tito 2:4 - Buku Lopatulika

4 kuti akalangize akazi aang'ono akonde amuna ao, akonde ana ao,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 kuti akalangize akazi aang'ono akonde amuna ao, akonde ana ao,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 kuti choncho athe kuphunzitsa azimai achitsikana kukonda amuna ao ndi ana ao.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Tsono atha kulangiza amayi achichepere kukonda amuna awo ndi ana awo.

Onani mutuwo Koperani




Tito 2:4
5 Mawu Ofanana  

Koma amasiye aang'ono uwakane; pakuti pamene ayamba kumchitira Khristu chipongwe afuna kukwatiwa;


Chifukwa chake nditi akwatiwe amasiye aang'ono, nabale ana, naweruzire nyumba, osapatsa chifukwa kwa mdaniyo chakulalatira;


akazi aakulu ngati amai; akazi aang'ono ngati alongo, m'kuyera mtima konse.


Momwemonso akazi okalamba akhale nao makhalidwe oyenera anthu oyera, osadierekeza, osakodwa nacho chikondi cha pavinyo, akuphunzitsa zokoma;


akhale odziletsa, odekha, ochita m'nyumba mwao, okoma, akumvera amuna a iwo okha, kuti mau a Mulungu angachitidwe mwano.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa