Numeri 9:12 - Buku Lopatulika12 Asasiyeko kufikira m'mawa, kapena kuthyolapo fupa; auchite monga mwa lemba lonse la Paska. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Asasiyeko kufikira m'mawa, kapena kuthyolapo fupa; auchite monga mwa lemba lonse la Paska. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Asasiyeko nyamayo mpaka m'maŵa kapena kuphwanya mafupa ake. Achite Paskayo potsata malamulo ake onse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Iwo asasiye nyama ina iliyonse mpaka mmawa. Asaswe mafupa aliwonse. Pamene akuchita chikondwerero cha Paska, atsate malangizo onse. Onani mutuwo |