Numeri 8:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo Mose ndi Aroni ndi khamu lonse la ana a Israele anachitira Alevi monga mwa zonse Yehova adauza Mose kunena za Alevi; momwemo ana a Israele anawachitira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo Mose ndi Aroni ndi khamu lonse la ana a Israele anachitira Alevi monga mwa zonse Yehova adauza Mose kunena za Alevi; momwemo ana a Israele anawachitira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Umu ndimo m'mene Mose ndi Aroni ndi mpingo wonse wa Aisraele, adaŵachitira Alevi. Aisraele adachitira Aleviwo zonse monga momwe Chauta adaalamulira Mose. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Mose, Aaroni pamodzi ndi gulu lonse la Israeli anachita kwa Alevi monga momwe Yehova analamulira Mose. Onani mutuwo |