Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 7:56 - Buku Lopatulika

56 chipande chimodzi chagolide cha masekeli khumi, chodzala ndi chofukiza;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

56 chipande chimodzi chagolide cha masekeli khumi, chodzala ndi chofukiza;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

56 Adaperekanso kambale kamodzi kagolide ka magaramu 110, kodzaza ndi lubani,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

56 mbale imodzi yagolide yolemera magalamu 110, yodzaza ndi lubani,

Onani mutuwo Koperani




Numeri 7:56
4 Mawu Ofanana  

Ndipo Aroni azifukizapo chofukiza cha zonunkhira zokoma m'mawa ndi m'mawa, pamene akonza nyalizo, achifukize.


Ndiponso miphika, ndi zoolera, ndi mbano zao, ndi mbale, ndi zipande, ndi zipangizo zonse zamkuwa zimene anatumikira nazo, anazichotsa.


chipande chimodzi chagolide cha masekeli khumi, chodzala ndi chofukiza;


chopereka chake ndicho mbale imodzi yasiliva, kulemera kwake masekeli zana limodzi ndi makumi atatu, mbale yowazira imodzi yasiliva ya masekeli makumi asanu ndi awiri, kuyesa sekeli wa malo opatulika; zonse ziwiri zodzala ndi ufa wosakaniza ndi mafuta, ukhale nsembe yaufa;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa