Numeri 7:44 - Buku Lopatulika44 chipande chimodzi chagolide cha masekeli khumi, chodzala ndi chofukiza; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201444 chipande chimodzi chagolide cha masekeli khumi, chodzala ndi chofukiza; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa44 Adaperekanso kambale kamodzi kagolide ka magaramu 110, kodzaza ndi lubani, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero44 mbale imodzi yagolide yolemera magalamu 110, yodzaza ndi lubani; Onani mutuwo |