Numeri 7:32 - Buku Lopatulika32 chipande chimodzi chagolide cha masekeli khumi, chodzala ndi chofukiza; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 chipande chimodzi chagolide cha masekeli khumi, chodzala ndi chofukiza; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Adaperekanso kambale kamodzi kagolide kolemera magaramu 110, kodzaza ndi lubani, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Mbale imodzi yagolide yolemera magalamu 110, yodzaza ndi lubani; Onani mutuwo |