Numeri 7:26 - Buku Lopatulika26 chipande chimodzi chagolide cha masekeli khumi, chodzala ndi chofukiza; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 chipande chimodzi chagolide cha masekeli khumi, chodzala ndi chofukiza; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Adaperekanso kambale kamodzi kagolide kolemera magaramu 110, kodzaza ndi lubani, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 mbale imodzi yagolide yolemera magalamu 110, yodzaza ndi lubani; Onani mutuwo |