Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 7:22 - Buku Lopatulika

22 tonde mmodzi akhale nsembe yauchimo;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 tonde mmodzi akhale nsembe yauchimo;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Adaperekanso tonde mmodzi woperekera nsembe yopepesera machimo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 mbuzi yayimuna imodzi ya nsembe yotetezera machimo;

Onani mutuwo Koperani




Numeri 7:22
3 Mawu Ofanana  

akamdziwitsa kuchimwa kwake adachimwako, azidza nacho chopereka chake, ndicho tonde wopanda chilema;


ng'ombe yamphongo imodzi, nkhosa yamphongo imodzi, mwanawankhosa mmodzi wa chaka chimodzi, zikhale nsembe yopsereza;


ndi nsembe yoyamika, ng'ombe ziwiri, nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu, anaankhosa asanu a chaka chimodzi; ndicho chopereka cha Netanele mwana wa Zuwara.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa