Numeri 6:27 - Buku Lopatulika27 Potero aike dzina langa pa ana a Israele; ndipo ndidzawadalitsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Potero aike dzina langa pa ana a Israele; ndipo ndidzawadalitsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Ndipo Chauta adati, “Akamadzatchula dzina langa podalitsa Aisraele, Ine ndidzaŵadalitsadi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Choncho akadzatchula dzina langa podalitsa Aisraeli, Ine ndidzawadalitsadi. Onani mutuwo |
Ndiponso mtundu uti wa padziko lapansi ufanana ndi anthu anu, ndiwo Israele, amene Mulungu anakadziombolera akhale anthu ake, ndi kuti limveke dzina lake, ndi kukuchitirani zinthu zazikulu ndi kuchitira dziko lanu zoopsa, pamaso pa anthu anu, amene munadziombolera kuwatulutsa ku dziko la Ejipito mwa amitundu ndi milungu yao?