Numeri 6:23 - Buku Lopatulika23 Nena ndi Aroni ndi ana ake, ndi kuti, Uzidalitsa ana a Israele motero; uziti nao, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Nena ndi Aroni ndi ana ake, ndi kuti, Uzidalitsa ana a Israele motero; uziti nao, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 “Uza Aroni ndi ana ake kuti azidalitsa Aisraele motere: Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 “Uza Aaroni ndi ana ake aamuna kuti, ‘Umu ndi mmene muzidalitsira Aisraeli. Muzinena kuti, Onani mutuwo |
Ndipo Aisraele onse, ndi akulu ao, ndi akapitao ao, ndi oweruza ao anaima chakuno ndi chauko cha likasa, pamaso pa ansembe Alevi, akusenza likasa la chipangano la Yehova, mbadwa ndi alendo omwe; ena a iwo pandunji paphiri la Gerizimu, ndi ena pandunji paphiri la Ebala; monga Mose, mtumiki wa Yehova, adalamulira poyamba paja kuti adalitse anthu a Israele.