Numeri 4:29 - Buku Lopatulika29 Kunena za ana a Merari, Uwawerenge monga mwa mabanja ao, monga mwa nyumba za makolo ao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Kunena za ana a Merari, Uwawerenge monga mwa mabanja ao, monga mwa nyumba za makolo ao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 “Uŵerenge ana a Merari potsata mabanja ao ndiponso banja la makolo ao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 “Werenga Amerari monga mwa mafuko awo ndi mabanja awo. Onani mutuwo |