Numeri 4:20 - Buku Lopatulika20 Koma asalowe kukaona zopatulikazo pozikulunga, kuti angafe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Koma asalowe kukaona zopatulikazo pozikulunga, kuti angafe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Koma asaloŵe kukayang'ana zinthu zopatulika mpang'ono pomwe, kuti angafe.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Koma Akohati asalowe kukaona zinthu zopatulika, ngakhale kanthawi pangʼono, chifukwa akatero adzafa.” Onani mutuwo |