Numeri 34:26 - Buku Lopatulika26 Wa fuko la ana a Isakara, kalonga Palatiele mwana wa Azani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Wa fuko la ana a Isakara, kalonga Palatiele mwana wa Azani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 M'fuko la ana a Isakara akhale Palatiele mwana wa Azani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Palitieli mwana wa Azani, mtsogoleri wochokera ku fuko la Isakara, Onani mutuwo |