Numeri 33:22 - Buku Lopatulika22 Nachokera Risa, nayenda namanga mu Kehelata. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Nachokera Risa, nayenda namanga m'Kehelata. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Adanyamuka ku Risa, nakamanga mahema ao ku Kehelata. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Atachoka ku Risa anakamanga ku Kehelata. Onani mutuwo |