Numeri 30:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo akakwatibwa naye mwamuna, pokhala ali nazo zowinda zake, kapena zonena zopanda pake za milomo yake, zimene anamanga nazo moyo wake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo akakwatibwa naye mwamuna, pokhala ali nazo zowinda zake, kapena zonena zopanda pake za milomo yake, zimene anamanga nazo moyo wake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Ngati mkazi alonjeza kapena alumbira mosaganiza bwino kuti adzachitadi kanthu kena, ndipo pambuyo pake akwatiwa, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 “Ngati akwatiwa atalumbira kale kapena ngati alonjeza mofulumira ndi pakamwa pake, Onani mutuwo |