Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 29:30 - Buku Lopatulika

30 ndi nsembe yake yaufa, ndi nsembe zake zothira, za ng'ombe, za nkhosa zamphongo, ndi za anaankhosa, monga mwa kuwerenga kwake, ndi kutsata lemba lake;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

30 ndi nsembe yake yaufa, ndi nsembe zake zothira, za ng'ombe, za nkhosa zamphongo, ndi za anaankhosa, monga mwa kuwerenga kwake, ndi kutsata lemba lake;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

30 pamodzi ndi chopereka cha chakudya ndi cha chakumwa pa ng'ombe zamphongo zija, pa nkhosa zamphongo zija, ndi pa anaankhosa aja, molingana ndi chiŵerengero cha nyamazo ndi potsata malangizo ake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

30 Pamodzi ndi ngʼombe zazimuna, nkhosa zazimuna ndi ana ankhosa, muzipereka chopereka cha chakudya ndi cha chakumwa molingana ndi chiwerengero cha nyamazo.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 29:30
2 Mawu Ofanana  

Ndi tsiku lachisanu ndi chimodzi ng'ombe zisanu ndi zitatu, nkhosa zamphongo ziwiri, anaankhosa khumi ndi anai, a chaka chimodzi, opanda chilema;


ndi tonde mmodzi akhale nsembe yauchimo; pamodzi ndi nsembe yopsereza yosalekeza, nsembe yake yaufa, ndi nsembe yake yothira.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa