Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 29:31 - Buku Lopatulika

31 ndi tonde mmodzi akhale nsembe yauchimo; pamodzi ndi nsembe yopsereza yosalekeza, nsembe yake yaufa, ndi nsembe yake yothira.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

31 ndi tonde mmodzi akhale nsembe yauchimo; pamodzi ndi nsembe yopsereza yosalekeza, nsembe yake yaufa, ndi nsembe yake yothira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

31 Muperekenso tonde mmodzi kuti akhale nsembe yopepesera machimo, kuwonjezera pa nsembe zopsereza za tsiku ndi tsiku zija, pamodzi ndi zopereka zake za chakudya ndi za chakumwa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

31 Muziperekenso mbuzi imodzi yayimuna ya nsembe yopepesera machimo, powonjezera pa nsembe yopsereza ya tsiku ndi tsiku pamodzi ndi chopereka chake cha chakudya ndi chakumwa.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 29:31
3 Mawu Ofanana  

ndiyo nsembe yopsereza ya tsiku la Sabata lililonse, pamodzi ndi nsembe yopsereza yosalekeza, ndi nsembe yake yothira.


ndi nsembe yake yaufa, ndi nsembe zake zothira, za ng'ombe, za nkhosa zamphongo, ndi za anaankhosa, monga mwa kuwerenga kwake, ndi kutsata lemba lake;


Ndi tsiku lachisanu ndi chiwiri ng'ombe zisanu ndi ziwiri, nkhosa zamphongo ziwiri, anaankhosa khumi ndi anai, a chaka chimodzi, opanda chilema;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa