Numeri 28:21 - Buku Lopatulika21 upereke limodzi la magawo khumi likhale la mwanawankhosa mmodzi; uzitero ndi anaankhosa asanu ndi awiri; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 upereke limodzi la magawo khumi likhale la mwanawankhosa mmodzi; uzitero ndi anaankhosa asanu ndi awiri; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 ndiponso wa makilogaramu limodzi pa mwanawankhosa aliyense. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Kilogalamu imodzi pa mwana wankhosa aliyense mwa ana ankhosa asanu ndi awiri aja. Onani mutuwo |