Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 23:30 - Buku Lopatulika

30 Ndipo Balaki anachita monga adanena Balamu, napereka ng'ombe ndi nkhosa yamphongo paguwa la nsembe lililonse.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

30 Ndipo Balaki anachita monga adanena Balamu, napereka ng'ombe ndi nkhosa yamphongo pa guwa la nsembe lililonse.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

30 Balaki adachitadi monga momwe adamuuzira Balamu, napereka ng'ombe yamphongo ndi nkhosa yamphongo pa guwa lililonse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

30 Balaki anachita monga Balaamu ananenera ndipo anapereka nsembe ngʼombe imodzi yayimuna ndi nkhosa imodzi yayimuna pa guwa lililonse.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 23:30
7 Mawu Ofanana  

Ndipo Abisalomu anaitana Ahitofele Mgiloni, phungu wa Davide, kumzinda wake ndiwo Gilo, pamene iye analikupereka nsembe. Ndipo chiwembucho chinali cholimba; pakuti anthu anachulukachulukabe kwa Abisalomu.


Chopereka chake chikakhala nsembe yopsereza ya ng'ombe, azibwera nayo yaimuna yopanda chilema; abwere nayo ku khomo la chihema chokomanako, kuti alandirike pamaso pa Yehova.


Pamenepo Balaki anapha ng'ombe ndi nkhosa, natumizira Balamu, ndi akalonga okhala naye.


Ndipo Balamu anati kwa Balaki, Ndimangireni kuno maguwa a nsembe asanu ndi awiri, nimundikonzere kuno ng'ombe zisanu ndi ziwiri, ndi nkhosa zamphongo zisanu ndi ziwiri.


Ndipo Balaki anachita monga Balamu ananena; ndipo Balaki ndi Balamu anapereka paguwa la nsembe lililonse ng'ombe ndi nkhosa yamphongo.


Ndipo Balamu anati kwa Balaki, Mundimangire pano maguwa a nsembe asanu ndi awiri, nimundikonzere pano ng'ombe zisanu ndi ziwiri, ndi nkhosa zamphongo zisanu ndi ziwiri.


Pamene Balamu anaona kuti kudakomera pamaso pa Yehova kudalitsa Israele, sanamuke, monga nthawi zina zija, ku nyanga zolodzera, koma anayang'ana nkhope yake kuchipululu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa