Numeri 21:22 - Buku Lopatulika22 Ndipitire pakati padziko lako; sitidzapatuka kulowa m'munda, kapena m'munda wampesa, sitidzamwako madzi a m'zitsime; tidzatsata mseu wachifumu, kufikira tapitirira malire ako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipitire pakati pa dziko lako; sitidzapatuka kulowa m'munda, kapena m'munda wampesa, sitidzamwako madzi a m'zitsime; tidzatsata mseu wachifumu, kufikira tapitirira malire ako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 “Mutilole kuti tidzere m'dziko mwanumo. Sitidzadzera m'minda mwanu, kapena m'mipesa mwanu. Sitidzamwa madzi a m'chitsime chanu. Tidzangotsata mseu wanu waukulu mpaka titadutsa dziko lanulo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 “Tiloleni kuti tidutse mʼdziko mwanu. Sitidzapatukira mʼminda mwanu kapena mu mpesa wanu kapena kumwa madzi mʼchitsime chili chonse. Tidzayenda mu msewu waukulu wa mfumu mpaka titadutsa malire a dziko lanu.” Onani mutuwo |