Numeri 20:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo khamulo linasowa madzi; pamenepo anasonkhana kutsutsana nao Mose ndi Aroni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo khamulo linasowa madzi; pamenepo anasonkhana kutsutsana nao Mose ndi Aroni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Kumeneko kunalibe madzi oti mpingowo umwe. Tsono anthu adasonkhana pamodzi naukira Mose ndi Aroni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Kunalibe madzi woti anthu onse ndi kumwa, choncho anthuwo anasonkhana motsutsana ndi Mose ndi Aaroni. Onani mutuwo |