Numeri 2:33 - Buku Lopatulika33 Koma sanawerenge Alevi mwa ana a Israele; monga Yehova adauza Mose. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Koma sanawerenge Alevi mwa ana a Israele; monga Yehova adauza Mose. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 Koma Alevi sadaŵaŵerengere kumodzi ndi Aisraele, monga momwe Chauta adaalamulira Mose. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 Koma Alevi sanawawerenge pamodzi ndi Aisraeli enawo monga momwe Yehova analamulira Mose. Onani mutuwo |