Numeri 19:5 - Buku Lopatulika5 Pamenepo atenthe ng'ombe yaikaziyo pamaso pake; atenthe chikopa chake ndi nyama yake, ndi mwazi wake, pamodzi ndi chipwidza chake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Pamenepo atenthe ng'ombe yamsotiyo pamaso pake; atenthe chikopa chake ndi nyama yake, ndi mwazi wake, pamodzi ndi chipwidza chake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Ng'ombeyo aitenthe, Eleazara akupenya. Chikopa chake, nyama yake, magazi ake pamodzi ndi ndoŵe yake, azitenthe zonsezo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Wansembeyo akuona, ngʼombeyo ayiwotche chikopa chake, mnofu wake, magazi ake ndi zamʼkati zake. Onani mutuwo |